Sunday, November 10, 2024
الرئيسيةLatestNthumwi 1200 za PDP zafika ku Blantyre

Nthumwi 1200 za PDP zafika ku Blantyre

Nthumwi zayamba kufika ku Comesa Hall mu mzinda wa Blantyre komwe chipani cha People’s Development (PDP) chikuchititsa msonkhano wake waukulu.

Yemwe akugwilizira udindo wa mneneri wa chipanichi a Rhodes Msonkho wati nthumwi zokwana 1200 ndi zomwe zikuyembekezeka kufika pa malowa.

A Msonkho atinso aitana zipani zina ku msonkhanowu. Mamembala ena a chipani cha Peoples (PP) afika kale.

Mtsogoleri wa chipanichi a Kondwani Nankhumwa, omwe alibe opikisana nawo, akuyembekezeka kutsekulira msonkhanowu.

TimesNkhani

مقالات ذات صلة

ترك الرد

من فضلك ادخل تعليقك
من فضلك ادخل اسمك هنا

- Advertisment -
Google search engine

الأكثر شهرة

احدث التعليقات